1 Mbiri 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Imbirani Yehova, inu nonse okhala padziko lapansi!+Tsiku ndi tsiku lengezani chipulumutso chimene amapereka!+ Salimo 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbani nyimbo zotamanda Yehova, inu okhulupirika ake,+Yamikani dzina lake loyera.*+ Salimo 147:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Imbirani Yehova molandizana mawu nyimbo zomuyamikira anthu inu.+Imbirani Mulungu wathu nyimbo zomutamanda ndi zeze.+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
23 Imbirani Yehova, inu nonse okhala padziko lapansi!+Tsiku ndi tsiku lengezani chipulumutso chimene amapereka!+
4 Imbani nyimbo zotamanda Yehova, inu okhulupirika ake,+Yamikani dzina lake loyera.*+ Salimo 147:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Imbirani Yehova molandizana mawu nyimbo zomuyamikira anthu inu.+Imbirani Mulungu wathu nyimbo zomutamanda ndi zeze.+
7 Imbirani Yehova molandizana mawu nyimbo zomuyamikira anthu inu.+Imbirani Mulungu wathu nyimbo zomutamanda ndi zeze.+