Yesaya 66:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mumzinda mukumveka phokoso lachisokonezo, phokoso lochokera kukachisi.+ Limeneli ndi phokoso losonyeza kuti Yehova akubwezera adani ake chilango chowayenerera.+ Ezekieli 33:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Dzikolo ndikadzalisandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka+ chifukwa cha zonyansa zonse zimene achita,+ iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’
6 Mumzinda mukumveka phokoso lachisokonezo, phokoso lochokera kukachisi.+ Limeneli ndi phokoso losonyeza kuti Yehova akubwezera adani ake chilango chowayenerera.+
29 Dzikolo ndikadzalisandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka+ chifukwa cha zonyansa zonse zimene achita,+ iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’