Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Komabe, anthuwo ananyamuka mwa iwo okha ulendo wopita kudera lamapiri kuja,+ koma likasa la pangano la Yehova silinachoke pakati pa msasa. Mose nayenso sanachoke.+

  • Yoswa 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ansembe 7 aziyenda patsogolo pa Likasa atanyamula malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo. Pa tsiku la 7 mudzagube kuzungulira mzindawo maulendo 7, ansembewo akuliza malipenga.+

  • 1 Samueli 14:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamenepo Sauli anauza Ahiya+ kuti: “Bweretsa likasa la Mulungu woona!”+ (Pakuti masiku amenewo likasa la Mulungu woona linali ndi ana a Isiraeli.)+

  • 2 Samueli 15:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno mfumu inauza Zadoki kuti: “Tenga likasa+ la Mulungu woona ndi kubwerera nalo mumzinda.+ Yehova akandikomera mtima adzandibwezeretsa mumzinda ndipo ndidzaliona. Ndidzaonanso malo amene limakhala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena