Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Atafika kumeneko anayamba kuliza lipenga la nyanga+ ya nkhosa m’dera lamapiri la Efuraimu.+ Iye ali patsogolo, ana a Isiraeli anatsika naye limodzi kuchoka m’dera lamapirilo.

  • Oweruza 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Amuna 300+ aja anapitiriza kuliza malipenga,+ ndipo Yehova anachititsa Amidiyani kuukirana okhaokha mumsasa wonsewo.+ Anthu onse a mumsasawo anathawa mpaka kukafika ku Beti-sita, ndi ku Zerera mpaka kumalire kwa mzinda wa Abele-mehola+ pafupi ndi Tabati.

  • 2 Samueli 2:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tsopano Yowabu analiza lipenga la nyanga ya nkhosa,+ ndipo anthu onse anaima, moti sanapitirizenso kuthamangitsa Isiraeli. Iwo sanayambirenso kumenyana.

  • Zefaniya 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pa tsiku limenelo, lipenga la nyanga ya nkhosa ndiponso chizindikiro chochenjeza zidzalira+ pochenjeza mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, komanso nsanja zazitali kwambiri za m’makona.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena