Yoswa 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Yoswa mwana wa Nuni anaitana ansembe+ n’kuwauza kuti: “Nyamulani likasa la pangano,+ ndipo ansembe 7 aziyenda patsogolo pa likasa+ la Yehovalo. Ansembewo atenge malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo.” Oweruza 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, iye anabweza amuna onse a Isiraeli koma anatsala ndi amuna 300 aja. Amenewa anatenga chakudya ndi malipenga a nyanga ya nkhosa+ m’manja mwa anthu amene anali kubwerera kwawo. Apa n’kuti msasa wa Amidiyani uli kumunsi kwawo, m’chigwa.+ Oweruza 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa m’magulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo m’mitsukomo anaikamo miyuni.
6 Chotero Yoswa mwana wa Nuni anaitana ansembe+ n’kuwauza kuti: “Nyamulani likasa la pangano,+ ndipo ansembe 7 aziyenda patsogolo pa likasa+ la Yehovalo. Ansembewo atenge malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo.”
8 Choncho, iye anabweza amuna onse a Isiraeli koma anatsala ndi amuna 300 aja. Amenewa anatenga chakudya ndi malipenga a nyanga ya nkhosa+ m’manja mwa anthu amene anali kubwerera kwawo. Apa n’kuti msasa wa Amidiyani uli kumunsi kwawo, m’chigwa.+
16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa m’magulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo m’mitsukomo anaikamo miyuni.