Yoswa 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ansembe 7 aziyenda patsogolo pa Likasa atanyamula malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo. Pa tsiku la 7 mudzagube kuzungulira mzindawo maulendo 7, ansembewo akuliza malipenga.+ Oweruza 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atafika kumeneko anayamba kuliza lipenga la nyanga+ ya nkhosa m’dera lamapiri la Efuraimu.+ Iye ali patsogolo, ana a Isiraeli anatsika naye limodzi kuchoka m’dera lamapirilo.
4 Ansembe 7 aziyenda patsogolo pa Likasa atanyamula malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo. Pa tsiku la 7 mudzagube kuzungulira mzindawo maulendo 7, ansembewo akuliza malipenga.+
27 Atafika kumeneko anayamba kuliza lipenga la nyanga+ ya nkhosa m’dera lamapiri la Efuraimu.+ Iye ali patsogolo, ana a Isiraeli anatsika naye limodzi kuchoka m’dera lamapirilo.