Salimo 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine ndinati: “Ngati simundiyankha adani anga adzasangalala chifukwa cha kusautsika kwanga.+Phazi langa likaterereka,+ iwo adzadzikweza pamaso panga.”+ Salimo 89:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mwakweza dzanja lamanja la adani ake.+Mwachititsa adani ake onse kusangalala.+
16 Ine ndinati: “Ngati simundiyankha adani anga adzasangalala chifukwa cha kusautsika kwanga.+Phazi langa likaterereka,+ iwo adzadzikweza pamaso panga.”+