-
2 Mafumu 8:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho Yehoramu anapita ku Zairi usiku pamodzi ndi magaleta ake onse. Kumeneko, iye ananyamuka usiku n’kukapha Aedomu amene anamuzungulira. Anaphanso akuluakulu oyang’anira asilikali okwera magaleta, ndipo anthu ena onse anathawira kumahema awo.
-