1 Mbiri 4:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pakati pawo panali ana ena a Simiyoni, amuna okwana 500, amene anapita kuphiri la Seiri.+ Atsogoleri awo anali Pelatiya, Neariya, Refaya, ndi Uziyeli ana a Isi. Ezekieli 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ‘Ine ndidzalanga Edomu kudzera mwa anthu anga Aisiraeli.+ Aisiraeliwo adzachitira Edomu mogwirizana ndi mkwiyo komanso ukali wanga, ndipo Aedomuwo adzadziwa mmene ndimalangira,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’
42 Pakati pawo panali ana ena a Simiyoni, amuna okwana 500, amene anapita kuphiri la Seiri.+ Atsogoleri awo anali Pelatiya, Neariya, Refaya, ndi Uziyeli ana a Isi.
14 ‘Ine ndidzalanga Edomu kudzera mwa anthu anga Aisiraeli.+ Aisiraeliwo adzachitira Edomu mogwirizana ndi mkwiyo komanso ukali wanga, ndipo Aedomuwo adzadziwa mmene ndimalangira,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’