Deuteronomo 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+ Salimo 58:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+ Nahumu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+ Chivumbulutso 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo anali kuuza mapiri ndi matanthwe mosalekeza kuti: “Tigwereni,+ tibiseni kuti tisaonekere kwa Iye amene wakhala pampando wachifumu,+ ndiponso kuti tibisike ku mkwiyo wa Mwanawankhosa,+
35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+
10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+
2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+
16 Iwo anali kuuza mapiri ndi matanthwe mosalekeza kuti: “Tigwereni,+ tibiseni kuti tisaonekere kwa Iye amene wakhala pampando wachifumu,+ ndiponso kuti tibisike ku mkwiyo wa Mwanawankhosa,+