Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Esau analinso kutchedwa Edomu.+ Deuteronomo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mtunda woyenda masiku 11 kuchokera ku Horebe kudzera njira ya kuphiri la Seiri yopita ku Kadesi-barinea.+
2 mtunda woyenda masiku 11 kuchokera ku Horebe kudzera njira ya kuphiri la Seiri yopita ku Kadesi-barinea.+