Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Esau analinso kutchedwa Edomu.+ Yoswa 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Isaki anabereka Yakobo ndi Esau.+ Pambuyo pake Esau ndinam’patsa phiri la Seiri kuti likhale lake.+ Kenako, Yakobo ndi ana ake anapita ku Iguputo.+
4 Isaki anabereka Yakobo ndi Esau.+ Pambuyo pake Esau ndinam’patsa phiri la Seiri kuti likhale lake.+ Kenako, Yakobo ndi ana ake anapita ku Iguputo.+