Genesis 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndipatseko chakudya chofiiracho pang’ono, icho chofiiracho! Ndatopatu ine!” Ndiye chifukwa chake anatchedwa Edomu.*+ Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Esau analinso kutchedwa Edomu.+
30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndipatseko chakudya chofiiracho pang’ono, icho chofiiracho! Ndatopatu ine!” Ndiye chifukwa chake anatchedwa Edomu.*+