Genesis 36:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mfumu Magidieli ndi Mfumu Iramu. Amenewa ndi amene anali mafumu a Edomu mogwirizana ndi madera awo mʼdziko lawo.+ Mibadwo ya Esau, kholo la Aedomu+ ndi imeneyi.
43 Mfumu Magidieli ndi Mfumu Iramu. Amenewa ndi amene anali mafumu a Edomu mogwirizana ndi madera awo mʼdziko lawo.+ Mibadwo ya Esau, kholo la Aedomu+ ndi imeneyi.