Genesis 36:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 mfumu Magidieli ndi mfumu Iramu. Amenewa ndiwo anali mafumu a Edomu+ monga mwa madera awo m’dziko lawo.+ Iyi ndiyo mibadwo ya Esau, kholo la Aedomu.+
43 mfumu Magidieli ndi mfumu Iramu. Amenewa ndiwo anali mafumu a Edomu+ monga mwa madera awo m’dziko lawo.+ Iyi ndiyo mibadwo ya Esau, kholo la Aedomu.+