Genesis 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndigawireko pangʼono mphodza zofiira zimene ukuphikazo,* ndatopatu ine!”* Nʼchifukwa chake anamupatsa dzina lakuti Edomu.*+ Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Dzina lina la Esau linali Edomu.+
30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndigawireko pangʼono mphodza zofiira zimene ukuphikazo,* ndatopatu ine!”* Nʼchifukwa chake anamupatsa dzina lakuti Edomu.*+