1 Samueli 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo chizindikiro chako chimene chidzachitikira ana ako awiri Hofeni ndi Pinihasi+ ndi ichi: Onse awiri adzafa tsiku limodzi.+ Salimo 78:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Ansembe ake anagwa ndi lupanga,+Ndipo akazi awo amasiye sanalire.+
34 Ndipo chizindikiro chako chimene chidzachitikira ana ako awiri Hofeni ndi Pinihasi+ ndi ichi: Onse awiri adzafa tsiku limodzi.+