1 Samueli 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anayamba kuuza Samueli kuti: “Tamvera! Ndichita+ zinazake mu Isiraeli zoti munthu aliyense akadzamva m’makutu ake onse mudzalira!+ 1 Samueli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero Afilisiti anamenyadi nkhondo, ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense wa iwo anayamba kuthawira kuhema wake.+ Ndipo amene anaphedwa anali ochuluka kwambiri.+ Panaphedwa amuna oyenda pansi a Isiraeli okwanira 30,000.+
11 Pamenepo Yehova anayamba kuuza Samueli kuti: “Tamvera! Ndichita+ zinazake mu Isiraeli zoti munthu aliyense akadzamva m’makutu ake onse mudzalira!+
10 Chotero Afilisiti anamenyadi nkhondo, ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense wa iwo anayamba kuthawira kuhema wake.+ Ndipo amene anaphedwa anali ochuluka kwambiri.+ Panaphedwa amuna oyenda pansi a Isiraeli okwanira 30,000.+