2 Mafumu 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa chifukwa chimenechi Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikubweretsa tsoka pa Yerusalemu+ ndi Yuda loti aliyense akamva, adzadabwa kwambiri.*+ Yeremiya 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova inu mafumu a Yuda ndi inu okhala mu Yerusalemu.+ Yehova wa makamu,+ Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “‘“Ine ndikubweretsa tsoka pamalo ano, ndipo aliyense akadzamva za tsoka limeneli, makutu ake adzalira.+
12 Pa chifukwa chimenechi Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikubweretsa tsoka pa Yerusalemu+ ndi Yuda loti aliyense akamva, adzadabwa kwambiri.*+
3 Ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova inu mafumu a Yuda ndi inu okhala mu Yerusalemu.+ Yehova wa makamu,+ Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “‘“Ine ndikubweretsa tsoka pamalo ano, ndipo aliyense akadzamva za tsoka limeneli, makutu ake adzalira.+