1 Samueli 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anayamba kuuza Samueli kuti: “Tamvera! Ndichita+ zinazake mu Isiraeli zoti munthu aliyense akadzamva m’makutu ake onse mudzalira!+ 2 Mafumu 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa chifukwa chimenechi Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikubweretsa tsoka pa Yerusalemu+ ndi Yuda loti aliyense akamva, adzadabwa kwambiri.*+
11 Pamenepo Yehova anayamba kuuza Samueli kuti: “Tamvera! Ndichita+ zinazake mu Isiraeli zoti munthu aliyense akadzamva m’makutu ake onse mudzalira!+
12 Pa chifukwa chimenechi Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikubweretsa tsoka pa Yerusalemu+ ndi Yuda loti aliyense akamva, adzadabwa kwambiri.*+