Yeremiya 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova inu mafumu a Yuda ndi inu okhala mu Yerusalemu.+ Yehova wa makamu,+ Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “‘“Ine ndikubweretsa tsoka pamalo ano, ndipo aliyense akadzamva za tsoka limeneli, makutu ake adzalira.+
3 Ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova inu mafumu a Yuda ndi inu okhala mu Yerusalemu.+ Yehova wa makamu,+ Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “‘“Ine ndikubweretsa tsoka pamalo ano, ndipo aliyense akadzamva za tsoka limeneli, makutu ake adzalira.+