Ekisodo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo usapange chilichonse chofanana ndi zifaniziro zawo,+ koma uzigwetse ndithu ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Danieli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ngati satipulumutsa, dziwani mfumu kuti ife sititumikira milungu yanu, ndipo sitilambira fano limene mwaimika.”+ 1 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiye chifukwa chake, okondedwa anga, thawani+ kupembedza mafano.+
24 Usaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo usapange chilichonse chofanana ndi zifaniziro zawo,+ koma uzigwetse ndithu ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+
18 Koma ngati satipulumutsa, dziwani mfumu kuti ife sititumikira milungu yanu, ndipo sitilambira fano limene mwaimika.”+