Levitiko 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+ 1 Samueli 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako amuna a ku Beti-semesi ananena kuti: “Ndani angaime pamaso pa Yehova Mulungu woyera,+ ndipo kodi sangatileke n’kupita kwa ena?”+ Salimo 99:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kwezani Yehova Mulungu wathu+ ndipo muweramireni pachopondapo mapazi ake.+Iye ndi woyera.+ Yesaya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aliyense anali kuuza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova wa makamu.+ Zonse zimene zili padziko lapansi zimasonyeza ulemerero wake.” 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma khalani motsanzira Woyera amene anakuitanani. Inunso khalani oyera m’makhalidwe anu onse,+
2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+
20 Kenako amuna a ku Beti-semesi ananena kuti: “Ndani angaime pamaso pa Yehova Mulungu woyera,+ ndipo kodi sangatileke n’kupita kwa ena?”+
3 Aliyense anali kuuza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova wa makamu.+ Zonse zimene zili padziko lapansi zimasonyeza ulemerero wake.”