Numeri 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano ana a Isiraeli anayamba kuuza Mose kuti: “Tsopano ife tifa ndithu! Ndithudi titha ife! Tonse titha basi.+ 2 Samueli 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Yehova,+ ndipo anati: “Kodi likasa la Yehova lidzabwera bwanji kumene ine ndikukhala?”+ 1 Mbiri 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Mulungu woona,+ ndipo anati: “Kodi ndibweretsa bwanji likasa la Mulungu woona kumene ine ndikukhala?”+ Salimo 76:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu ndinu wochititsa mantha,+Ndani angaime pamaso panu inu mutakwiya kwambiri?+
12 Tsopano ana a Isiraeli anayamba kuuza Mose kuti: “Tsopano ife tifa ndithu! Ndithudi titha ife! Tonse titha basi.+
9 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Yehova,+ ndipo anati: “Kodi likasa la Yehova lidzabwera bwanji kumene ine ndikukhala?”+
12 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Mulungu woona,+ ndipo anati: “Kodi ndibweretsa bwanji likasa la Mulungu woona kumene ine ndikukhala?”+