1 Mbiri 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Davide anachita mantha kwambiri ndi Mulungu woona tsiku limenelo ndipo anati: “Ndiye ndilitenga bwanji Likasa la Mulungu woona nʼkupita nalo kumene ine ndikukhala?”+
12 Choncho Davide anachita mantha kwambiri ndi Mulungu woona tsiku limenelo ndipo anati: “Ndiye ndilitenga bwanji Likasa la Mulungu woona nʼkupita nalo kumene ine ndikukhala?”+