1 Mbiri 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Mulungu woona,+ ndipo anati: “Kodi ndibweretsa bwanji likasa la Mulungu woona kumene ine ndikukhala?”+
12 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Mulungu woona,+ ndipo anati: “Kodi ndibweretsa bwanji likasa la Mulungu woona kumene ine ndikukhala?”+