2 Samueli 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Yehova,+ ndipo anati: “Kodi likasa la Yehova lidzabwera bwanji kumene ine ndikukhala?”+
9 Tsiku limenelo, Davide anachita mantha kwambiri chifukwa cha Yehova,+ ndipo anati: “Kodi likasa la Yehova lidzabwera bwanji kumene ine ndikukhala?”+