Deuteronomo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu anakhala mfumu mu Yesuruni,*+Pamene atsogoleri a anthu anasonkhana pamodzi,+Chiwerengero chonse cha mafuko a Isiraeli.+ Salimo 74:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+ Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+ Chivumbulutso 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+
5 Mulungu anakhala mfumu mu Yesuruni,*+Pamene atsogoleri a anthu anasonkhana pamodzi,+Chiwerengero chonse cha mafuko a Isiraeli.+
12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+
22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+
17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+