Ekisodo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mphamvu ndi nyonga yanga ndi Ya,*+ pakuti wandipulumutsa.+Ameneyu ndi Mulungu wanga, ndidzam’tamanda.+ Ndiye Mulungu wa atate anga,+ ndidzam’kweza.+ Habakuku 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munapita kuti mukapulumutse anthu anu,+ kuti mukapulumutse wodzozedwa wanu. Munaphwanyaphwanya mtsogoleri wa nyumba ya wochimwa.+ Nyumbayo inafafanizidwa mpaka kudenga moti maziko a nyumbayo anaonekera.+ [Seʹlah.]
2 Mphamvu ndi nyonga yanga ndi Ya,*+ pakuti wandipulumutsa.+Ameneyu ndi Mulungu wanga, ndidzam’tamanda.+ Ndiye Mulungu wa atate anga,+ ndidzam’kweza.+
13 Munapita kuti mukapulumutse anthu anu,+ kuti mukapulumutse wodzozedwa wanu. Munaphwanyaphwanya mtsogoleri wa nyumba ya wochimwa.+ Nyumbayo inafafanizidwa mpaka kudenga moti maziko a nyumbayo anaonekera.+ [Seʹlah.]