Salimo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ngalande za pansi pa madzi zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi anakhala poonekera.+Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwanu.+ Ezekieli 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Khoma limene amuna inu mwalipaka laimulo, ndidzaligwetsa lonse mpaka pansi moti maziko ake adzaonekera.+ Mzindawo udzawonongedwa ndithu, ndipo inuyo mudzathera pakati pake. Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
15 Ndipo ngalande za pansi pa madzi zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi anakhala poonekera.+Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwanu.+
14 Khoma limene amuna inu mwalipaka laimulo, ndidzaligwetsa lonse mpaka pansi moti maziko ake adzaonekera.+ Mzindawo udzawonongedwa ndithu, ndipo inuyo mudzathera pakati pake. Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+