Salimo 74:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndinu amene munang’amba nthaka ndi kupanga akasupe ndi makwawa.+Inu munaumitsa mitsinje imene inali kukhala ndi madzi nthawi zonse.+ Salimo 106:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho anadzudzula Nyanja Yofiira, ndipo pang’onopang’ono nyanjayo inauma.+Pamenepo anawayendetsa kudutsa pakati pa madzi akuya ngati akuwayendetsa m’chipululu.+ Salimo 114:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyanja inaona ndipo inathawa.+Yorodano anabwerera m’mbuyo.+
15 Ndinu amene munang’amba nthaka ndi kupanga akasupe ndi makwawa.+Inu munaumitsa mitsinje imene inali kukhala ndi madzi nthawi zonse.+
9 Choncho anadzudzula Nyanja Yofiira, ndipo pang’onopang’ono nyanjayo inauma.+Pamenepo anawayendetsa kudutsa pakati pa madzi akuya ngati akuwayendetsa m’chipululu.+ Salimo 114:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyanja inaona ndipo inathawa.+Yorodano anabwerera m’mbuyo.+