Nehemiya 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munagawa nyanja+ pamaso pawo ndipo iwo anadutsa panthaka youma pakati pa nyanja.+ Anthu amene anali kuwathamangitsa munawaponya m’nyanja yozama+ ngati mwala+ woponyedwa m’madzi amphamvu.+ Salimo 77:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Msewu wanu unadutsa panyanja,+Ndipo njira yanu inadutsa pamadzi ambiri.Mmene mapazi anu anaponda simunaoneke. Salimo 136:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amenenso anachititsa Isiraeli kudutsa pakati pake:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Yesaya 63:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 amene anawawolotsa pamadzi amphamvu moti sanapunthwe, mofanana ndi hatchi m’chipululu?+
11 Munagawa nyanja+ pamaso pawo ndipo iwo anadutsa panthaka youma pakati pa nyanja.+ Anthu amene anali kuwathamangitsa munawaponya m’nyanja yozama+ ngati mwala+ woponyedwa m’madzi amphamvu.+
19 Msewu wanu unadutsa panyanja,+Ndipo njira yanu inadutsa pamadzi ambiri.Mmene mapazi anu anaponda simunaoneke.
14 Amenenso anachititsa Isiraeli kudutsa pakati pake:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Yesaya 63:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 amene anawawolotsa pamadzi amphamvu moti sanapunthwe, mofanana ndi hatchi m’chipululu?+