2 Samueli 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo ngalande za pansi pa nyanja zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi+ anakhala poonekera,Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwa Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwake.+ Salimo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzaweruza anthu padziko lapansi mwachilungamo.+Adzazenga mlandu mitundu ya anthu moyenerera.+
16 Ndipo ngalande za pansi pa nyanja zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi+ anakhala poonekera,Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwa Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwake.+