Yoswa 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yoswa analanda mizinda yonse ya mafumuwa, ndi kugwira mafumu onse a mizindayi n’kuwapha ndi lupanga.+ Anawawononga onsewo+ monga mmene analamulira Mose mtumiki wa Yehova.+ Salimo 68:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndithudi, Mulungu adzaphwanya mitu ya adani ake kukhala zibenthuzibenthu,+Adzaphwanya liwombo latsitsi la aliyense woyenda m’njira yochimwa.+ Salimo 110:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+
12 Yoswa analanda mizinda yonse ya mafumuwa, ndi kugwira mafumu onse a mizindayi n’kuwapha ndi lupanga.+ Anawawononga onsewo+ monga mmene analamulira Mose mtumiki wa Yehova.+
21 Ndithudi, Mulungu adzaphwanya mitu ya adani ake kukhala zibenthuzibenthu,+Adzaphwanya liwombo latsitsi la aliyense woyenda m’njira yochimwa.+
6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+