Salimo 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndiye mphamvu kwa anthu ake,+Iye ndi malo achitetezo odzetsa chipulumutso chachikulu kwa wodzozedwa wake.+ Salimo 68:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu, pamene munatsogolera anthu anu,+Pamene munadutsa m’chipululu,+ [Seʹlah.]
8 Yehova ndiye mphamvu kwa anthu ake,+Iye ndi malo achitetezo odzetsa chipulumutso chachikulu kwa wodzozedwa wake.+