Salimo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,+Amamupulumutsa ndi dzanja lake lamanja lamphamvu zopulumutsa.+ Aheberi 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene anali munthu, Khristu anapereka mapemphero opembedzera ndi opempha,+ kwa amene anali wokhoza kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula+ komanso akugwetsa misozi, ndipo anamumvera chifukwa chakuti anali kuopa Mulungu.+
6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,+Amamupulumutsa ndi dzanja lake lamanja lamphamvu zopulumutsa.+
7 Pamene anali munthu, Khristu anapereka mapemphero opembedzera ndi opempha,+ kwa amene anali wokhoza kumupulumutsa ku imfa. Anapereka mapempherowa mofuula+ komanso akugwetsa misozi, ndipo anamumvera chifukwa chakuti anali kuopa Mulungu.+