Salimo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sonyezani kukoma mtima kosatha mwa kuchita zodabwitsa,+ inu Mpulumutsi wa anthu othawira kwa inu,Amene akuthawa anthu ogalukira dzanja lanu lamanja.+
7 Sonyezani kukoma mtima kosatha mwa kuchita zodabwitsa,+ inu Mpulumutsi wa anthu othawira kwa inu,Amene akuthawa anthu ogalukira dzanja lanu lamanja.+