Salimo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+ Salimo 105:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+ Luka 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?
2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+ Salimo 105:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+ Luka 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?
15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+
7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?