Salimo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+ Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,Pomupulumutsa modabwitsa ndi dzanja lake lamanja.+
6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+ Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,Pomupulumutsa modabwitsa ndi dzanja lake lamanja.+