Salimo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,+Amamupulumutsa ndi dzanja lake lamanja lamphamvu zopulumutsa.+
6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,+Amamupulumutsa ndi dzanja lake lamanja lamphamvu zopulumutsa.+