-
Numeri 1:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Amenewa ndi amene analembedwa mayina, amene Mose ndi Aroni anawawerenga mothandizidwa ndi atsogoleri 12, amuna achiisiraeli. Aliyense wa amunawa anaimira nyumba za makolo ake.
-