Genesis 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 koma sanakondwere naye Kaini ndi nsembe yake+ m’pang’ono pomwe. Chotero Kaini anapsa mtima kwambiri+ ndipo nkhope yake inagwa. Genesis 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+ 1 Yohane 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 osati ngati Kaini, amene anachokera kwa woipayo n’kupha+ m’bale wake. N’chifukwa chiyani iye anapha m’bale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za m’bale wake zinali zolungama.+
5 koma sanakondwere naye Kaini ndi nsembe yake+ m’pang’ono pomwe. Chotero Kaini anapsa mtima kwambiri+ ndipo nkhope yake inagwa.
8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+
12 osati ngati Kaini, amene anachokera kwa woipayo n’kupha+ m’bale wake. N’chifukwa chiyani iye anapha m’bale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za m’bale wake zinali zolungama.+