Numeri 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Balaki+ mwana wa Zipori, anaona zonse zimene Aisiraeli anachita kwa Aamori.