9 Kenako Balaki mwana wa Zipori,+ mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Isiraeli.+ Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori, ndi kumuuza kuti akutemberereni.+
25 Tsopano kodi iweyo wasiyana pati ndi Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu?+ Kodi iye anakwanitsa kulimbana ndi Isiraeli, kapena kuyesa kumenyana naye?