Numeri 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Balaki+ mwana wa Zipori, anaona zonse zimene Aisiraeli anachita kwa Aamori. Deuteronomo 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Muamoni kapena Mmowabu asalowe mumpingo wa Yehova.+ Ana awo asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10, ngakhalenso mpaka kalekale. Yoswa 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Balaki mwana wa Zipori,+ mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Isiraeli.+ Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori, ndi kumuuza kuti akutemberereni.+
3 “Muamoni kapena Mmowabu asalowe mumpingo wa Yehova.+ Ana awo asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10, ngakhalenso mpaka kalekale.
9 Kenako Balaki mwana wa Zipori,+ mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Isiraeli.+ Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori, ndi kumuuza kuti akutemberereni.+