Hoseya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Zimene zidzachitikira anthuwo zidzachitikiranso ansembe.+ Ndidzawaimba mlandu onsewa chifukwa cha njira zawo+ ndipo ndidzawabwezera zochita zawo.+
9 “Zimene zidzachitikira anthuwo zidzachitikiranso ansembe.+ Ndidzawaimba mlandu onsewa chifukwa cha njira zawo+ ndipo ndidzawabwezera zochita zawo.+