Hoseya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova ali ndi mlandu woti aimbe Yuda.+ Adzalanga Yakobo mogwirizana ndi njira zake+ ndipo adzamubwezera mogwirizana ndi zochita zake.+ Amosi 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+ Aroma 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero aliyense wa ife adzayankha yekha kwa Mulungu.+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+
2 “Yehova ali ndi mlandu woti aimbe Yuda.+ Adzalanga Yakobo mogwirizana ndi njira zake+ ndipo adzamubwezera mogwirizana ndi zochita zake.+
2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+