Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 17:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Komabe, nawonso Ayudawo sanasunge malamulo a Yehova Mulungu+ wawo, koma anayenda motsatira malamulo amene Aisiraeli+ anapanga.

  • Yeremiya 2:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 “Koma iwe ukuti, ‘Ine ndilibe mlandu uliwonse. Ndithudi mkwiyo wake wandichokera.’+

      “Tsopano ndikuyamba kukuimba mlandu chifukwa chonena kuti, ‘Sindinachimwe.’+

  • Hoseya 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tamverani mawu a Yehova inu ana a Isiraeli. Yehova ali ndi mlandu ndi anthu okhala m’dzikoli,+ chifukwa m’dzikoli mulibe choonadi,+ kukoma mtima kosatha, ndiponso anthu a m’dzikoli amachita zinthu ngati kuti sadziwa Mulungu.+

  • Mika 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Inu mapiri, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake. Inu matanthwe okhazikika, tamverani. Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+ pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake. Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena