Yeremiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+ Aroma 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+
22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+
28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+