Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+

      Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+

      Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+

      Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+

  • Salimo 50:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Wamphamvuyo,+ Yehova, Mulungu,+ walankhula+

      Ndipo akuitana dziko lapansi,+

      Kuchokera kotulukira dzuwa mpaka kumene limalowera.+

  • Miyambo 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 pamene anaikira nyanja lamulo lake lakuti madzi ake asapitirire pamene anawalamula,+ pamene anakhazikitsa maziko a dziko lapansi,+

  • Yesaya 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+

  • Yeremiya 31:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Yehova wanena kuti: “‘Ngati kumwamba kungayezedwe ndipo ngati maziko a dziko lapansi angafufuzidwe,+ inenso ndingakane anthu onse amene ndi mbewu ya Isiraeli chifukwa cha zonse zimene achita,’+ watero Yehova.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena